Leviticus 14:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Wansembe atapeko mafuta pang'ono, nkuŵathira m'dzanja lake lakumanzere.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo wansembe atengeko muyeso uja wa mafuta, nawathire pa chikhato cha dzanja lake lamanzere la iye mwini;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wansembe atengeko mafuta pangʼono, nʼkuwathira mʼdzanja lake lamanzere,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo wansembe atengeko muyeso wa mafuta, nawathire pa cikhato ca dzanja lace lamanzere la iye mwini;