Leviticus 14:2 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Lamulo la munthu wakhate pa tsiku la kuyeretsedwa kwake nali: Abwere naye kwa wansembe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chilamulo cha wakhate tsiku la kumyeretsa kwake ndi ichi: azidza naye kwa wansembe;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Malamulo a munthu wakhate pa tsiku la kuyeretsedwa kwake ndi awa: Abwere naye kwa wansembe.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cilamulo ca wakhate tsiku la kumyeretsa kwace ndi ici: azidza naye kwa wansembe;