Leviticus 14:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono malinga ndi m'mene adapezeramo, apereke njiŵa ziŵiri kapena maundaankhunda aŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye apereke imodzi ya njiwazo, kapena limodzi la maunda, monga akhoza kufikana nazo,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndipo munthuyo apereke njiwa ziwiri kapena mawunda ankhunda awiri, molingana ndi mmene anapezeramo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye apereke imodzi ya njiwazo, kapena limodzi la maunda, monga akhoza kufikana nazo, limodzi la nsembe yaucimo, ndi tina la nsembe yopsereza, pamodzi ndi nsembe yaufa;