Leviticus 14:32 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Limeneli ndilo lamulo la munthu wakhate amene alibe zinthu zoperekera kuyeretsedwa kwake.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi ndi chilamulo cha iye ali ndi nthenda yakhate, wosakhoza kufikana nazo zofunika pomyeretsa pake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Amenewa ndi malamulo a munthu wakhate amene alibe zinthu zoti apereke pamene akuyeretsedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ndi cilamulo ca iye ali ndi nthenda yakhate, wosakhoza kufikana nazo zofunika pomyeretsa pace.