Leviticus 14:37 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo aonetsetse nderezo. Akapezeka kuti zili m'khoma la nyumba, niziwoneka ndi maanga achisipu kapena ofiira, ndipo ikaoneka kuti yaloŵera mpaka m'kati,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
naone nthendayo, ndipo taonani, nthenda ikakhala yosumbudzuka m'makoma a nyumba yobiriwira kapena yofiira, ndipo maonekedwe ake yakumba kubzola khoma;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye aonetsetse nderezo. Tsono akapeza kuti nderezo zili mʼkhoma la nyumba, ndipo ngati zili ndi mawanga obiriwira kapena ofiirira, komanso zikuoneka kuti zalowerera mpaka mʼkati mwa khoma,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
naone nthendayo, ndipo taonani, nthenda ikakhala yosumbudzuka m'makoma a nyumba yobiriwira kapena yofiira, ndipo maonekedwe ace yakumba kubzola khoma;