Leviticus 14:39 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pa tsiku lachisanu ndi chiŵiri wansembeyo abwerenso kudzayang'ana. Nderezo zikakhala kuti zafalikira m'makoma a nyumbayo,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo wansembe abwerenso tsiku lachisanu ndi chiwiri, naonenso, ndipo taonani, ngati nthenda yakula m'makoma a nyumba;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pa tsiku la chisanu ndi chiwiri wansembe abwerenso kudzayangʼana mʼnyumbamo. Ngati ndere yafalikira mʼmakoma a nyumbayo,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo wansembe abwerenso tsiku lacisanu ndi ciwiri, naonenso, ndipo taonani, ngati nthenda yakula m'makoma a nyumba;