Leviticus 14:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
wansembe alamule anthu kuti wodwala amene akuti ayeretsedweyo, amtengere mbalame zamoyo ziŵiri zimene Ayuda amaloledwa kudya, nthambi yamkungudza, kansalu kamlangali ndi kanthambi ka hisope.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
pamenepo wansembe auze kuti amtengere iye wakuti akonzedwe, mbalame ziwiri zoyera zamoyo, ndi mtengo wamkungudza, ndi ubweya wofiira, ndi hisope;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
wansembe alamule anthu kuti amutengere wodwala woti ayeretsedweyo, mbalame zamoyo ziwiri zomwe Ayuda amaloledwa kudya, nthambi yamkungudza, kansalu kofiirira ndi kanthambi ka hisope.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
pamenepo wansembe auze kuti amtengere iye wakuti akonzedwe, mbalame ziwiri zoyera zamoyo, ndi mtengo wamkungudza, ndi, ubweya wofiira, ndi hisope;