Leviticus 14:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono anthuwo atenge miyala ina ndi kuiloŵetsa m'malo mwa miyala adagumula ija, mwiniwakeyo atengenso dothi lina ndipo amate nyumbayo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
natenge miyala ina, naikhazike m'malo mwa miyala ija; natenge dothi lina, namatenso nyumbayo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono anthuwo atenge miyala ina ndi kuyilowetsa mʼmalo mwa miyala imene anagumula ija ndipo atenge dothi latsopano ndi kumata nyumbayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
natenge miyala yina, naikhazike m'male mwa miyala ija; natenge dothi tina, namatenso nyumbayo.