Leviticus 14:54 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Izi ndizo zimene muyenera kuchita ngati muona kuti
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi ndi chilamulo cha nthenda iliyonse yakhate, ndi yamfundu;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amenewa ndiwo malamulo a nthenda ya khate, bala lonyerenyetsa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ndi cilamulo ca nthenda iri yonse yakhate, ndi yamfundu;