Leviticus 14:57 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malamulo ameneŵa ngonena za chinthu choipitsidwa ndi chosaipitsidwa. Atsatidwe pa nthenda zonse za khate.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
kulangiza tsiku loti chikhala chodetsa, ndi tsiku loti chikhala choyera; ichi ndi chilamulo cha khate.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
kuti mudziwe ngati chinthucho ndi choyeretsedwa kapena chodetsedwa. Amenewa ndiwo malamulo a nthenda zonse za khate.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
kulangiza tsiku loti cikhala codetsa, ndi tsiku loti cikhala coyera; ici ndi cilamulo ca khate.