Leviticus 14:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono wansembe awaze magazi kasanu ndi kaŵiri pa munthu amene akuti amuyeretse khateyo. Pamenepo wodwalayo amutche kuti ndi woyeretsedwa, ndipo aiwulutsire ku thengo mbalame yamoyoyo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
nawaze kasanu ndi kawiri iye amene akuti amyeretse khate lake, namutche woyera, nataye mbalame yamoyo padambo poyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Wansembe awaze magazi kasanu ndi kawiri pa munthu woti amuyeretse khateyo ndipo alengeze kuti munthuyo ndi woyeretsedwa. Kenaka wansembe awulutsire ku thengo mbalame yamoyoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
nawaze kasanu ndi kawiri iye amene akuti amyeretse khate lace, namuche woyera, nataye mbalame yamoyo padambo poyera.