Leviticus 15:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Mwamuna akataya pansi mbeu yake yaumuna, asambe thupi lake lonse koma akhalabe woipitsidwa mpaka madzulo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munthu aliyense akagona uipa, azisamba thupi lake lonse ndi madzi, nadzakhala wodetsedwa kufukira madzulo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Mwamuna akataya pansi mbewu yake yaumuna, asambe thupi lake lonse. Komabe adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munthu ali yense akagona uipa, azisamba thupi lace lonse ndi madzi, nadzakhala wodetsedwa kufikira madzulo.