Leviticus 15:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Muuze Aisraele kuti: Mwamuna aliyense akakhala ndi nthenda yotulutsa mafinya ku maliseche ake, zimenezo nzonyansa ndithu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nenani nao ana a Israele, nimuti nao, Pamene mwamuna aliyense ali ndi nthenda yakukha m'thupi mwake, akhale wodetsedwa, chifukwa cha kukha kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Yankhulani ndi Aisraeli ndipo muwawuze kuti, ‘Mwamuna aliyense akakhala ndi nthenda yotulutsa mafinya ku maliseche ake, zotulukazo ndi zonyansa ndithu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nenani nao ana a Israyeli, nimuti nao, Pamene mwamuna ali yense ali ndi nthenda yakukha m'thupi mwace, akhale wodetsedwa, cifukwaca kukha kwace.