Leviticus 15:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Atatha matenda a kusamba kwakeko, mkazi aŵerenge masiku asanu ndi aŵiri, ndipo pambuyo pake akhala woyeretsedwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma akayeretsedwa kukha kwake, adziwerengere masiku asanu ndi awiri, ndipo atatero adzakhala woyeretsedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Nthawi yosamba ikatha, mkaziyo awerenge masiku asanu ndi awiri, ndipo masikuwo akatha adzakhala woyeretsedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma akayeretsedwa kukha kwace, adziwerengere masiku asanu ndi awiri, ndipo atatero adzakhala woyeretsedwa.