Leviticus 15:32 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lamulo limeneli ndi la mwamuna amene ali ndi nthenda yotulutsa mafinya m'thupi mwake, ndiponso la amene ataya pansi mbeu yake yaumuna, imene imamsandutsa woipitsidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ichi ndi chilamulo cha wakukha, ndi cha iye wakugona uipa, kuti kumkhalitse wodetsedwa;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Amenewa ndi malamulo a munthu amene akutuluka mafinya kumaliseche kwake, komanso a munthu aliyense amene wadetsedwa ndi mbewu yaumuna,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ici ndi cilamulo ca wakukha, ndi ca iye wakugona uipa, kuti kumkhalitse wodetsedwa;