Leviticus 15:33 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Lamulo limenelinso ndi la mkazi amene ali ndi matenda osamba. Lamuloli ndi la aliyense, mwamuna kapena mkazi, amene ali ndi nthenda yotulutsa mafinya kumaliseche kwake, ndiponso la mwamuna amene agona ndi mkazi woipitsidwa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi cha mkazi alinkudwala ndi kudetsedwa kwake, ndi cha iye alikukha kapena mwamuna, kapena mkazi, ndi cha iye agona ndi mkazi wodetsedwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mkazi wodwala chifukwa cha msambo komanso a mwamuna kapena mkazi amene akutulutsa mafinya kumaliseche kwake ndi mwamuna wogona ndi mkazi amene akusamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi ca mkazi alinkudwala ndi kudetsedwa kwace, ndi ca iye alikukha kapena mwamuna, kapena mkazi, ndi ca iye agona ndi mkazi wodetsedwa.