Leviticus 16:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Awazeko magazi ena pamwamba pa guwalo ndi chala chake kasanu ndi kaŵiri, kuti alipatule ndi kuliyeretsa pochotsa machimo a Aisraele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo awazepo mwazi wina ndi chala chake kasanu ndi katatu; ndi kuliyeretsa ndi kulipatula kulichotsera zodetsa za ana a Israele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Magazi ena awawaze pa guwalo ndi chala chake kasanu ndi kawiri kuliyeretsa ndi kulipatula kuchotsa zodetsa za Aisraeli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo awazepo mwazi wina ndi cala cace kasanu ndi katatu; ndi kuliyeretsa ndi kulipatula kulicotsera zodetsa za ana a Israyeli.