Leviticus 16:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mbuziyo isenze machimo ao onse ndi kumanka nawo ku chipululu. Munthuyo aileke mbuzi imeneyo kuti ipite ku chipululu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi mbuziyo isenze yokha mphulupulu zonsezo kunka nazo ku dziko la pa lokha; ndipo azitaya mbuziyo m'chipululu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mbuziyo isenze machimo awo onse ndi kupita nawo kutali ndipo munthuyo aleke mbuziyo kuti ipite ku chipululuko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi mbuziyo isenze yokha mphulupulu zonsezo kumka nazo ku dziko la pa lokha; ndipo azitaya mbuziyo m'cipululu.