Leviticus 17:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Nchifukwa chake ndaŵauza Aisraele kuti munthu aliyense mwa inu, kapena mlendo wokhala pakati panu, asadye magazi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa chake ndinanena kwa ana a Israele, Asamadya mwazi mmodzi yense wa inu, kapena mlendo aliyense wakugonera mwa inu asamadya mwazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho ndikuwawuza Aisraeli kuti, ‘Pasapezeke aliyense wa inu wodya magazi, ngakhale mlendo wokhala pakati panu.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa cace ndinanena kwa ana a Israyeli, Asamadya mwazi mmodzi yense wa inu, kapena mlendo ali yense wakugoneramwa inu asamadya mwazi.