Leviticus 17:16 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma akapanda kuchapa zovalazo, kapena akapanda kusamba thupi lonse, adzasenza machimo ake.’ ”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma akapanda kuzitsuka, kapena kusamba thupi lake, adzasenza mphulupulu yake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma ngati sachapa zovala zake ndi kusamba, adzasenzabe machimo ake.’ ”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma akapanda kuzitsuka, kapena kusamba thupi lace, adzasenza mpholupulu yace.