Leviticus 17:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uza Aroni ndi ana ake, pamodzi ndi Aisraele onse, kuti Chauta akulamula kuti,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nena ndi Aroni, ndi ana ake amuna, ndi ana a Israele onse, nuti nao, Ichi ndi chimene Yehova wauza, ndi kuti,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Uza Aaroni ndi ana ake, pamodzi ndi Aisraeli onse kuti, ‘Chimene Yehova walamula ndi ichi:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nena ndi Aroni, ndi ana ace amuna, ndi ana a Israyeli onse, nuti nao, Ici ndi cimene Yehova wauza, ndi kuti,