Leviticus 17:3 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
‘Mwisraele aliyense akapha ng'ombe, kapena mwanawankhosa, kapena mbuzi, ku zithando kapena kunja kwa zithando,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu aliyense wa mbumba ya Israele akapha ng'ombe, kapena mwanawankhosa, kapena mbuzi, m'chigono, kapena akaipha kunja kwa chigono,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwisraeli aliyense amene apha ngʼombe, mwana wankhosa kapena mbuzi mu msasa kapena kunja kwa msasa,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu ali yense wa mbumba ya Israyeli akapha ng'ombe, kapena mwana wa nkhosa, kapena mbuzi, m'cigono, kapena akaipha kunja kwa cigono,