Leviticus 17:4 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
koma osabwera nayo pa khomo pa chihema chamsonkhano, kuti ikhale mphatso yopereka kwa Chauta, munthuyo wapalamula mlandu wa magazi, chifukwa wakhetsa magazi. Munthu ameneyo achotsedwe pakati pa anthu anzake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
osadza nayo ku khomo la chihema chokomanako, kuti aipereke chopereka cha Yehova, ku bwalo la Kachisi wa Yehova; azimuyesa munthuyu wochimwira mwazi, wakhetsa mwazi; ndipo amsadze munthuyo kumchotsa pakati pa anthu a mtundu wake;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
mʼmalo mobwera nayo pa khomo la tenti ya msonkhano pamaso pa Yehova ndi kuyipereka kuti ikhale nsembe ya Yehova, ameneyo wapalamula mlandu wa magazi, wakhetsa magazi ndipo ayenera kuchotsedwa pakati pa anthu anzake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
osadza nayo ku khomo la cihema cokomanako, kuti aipereke copereka ca Yehova, ku bwalo la kacisi wa Yehova; azimuyesa munthuyu wocimwira mwazi, wakhetsa mwazi; ndipo amsadze munthuyo kumcotsa pakati pa anthu a mtundu wace;