Leviticus 18:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usagone ndi mdzukulu wako, mwana wa mwana wako wamwamuna, kapena mdzukulu wako, mwana wa mwana wako wamkazi, chifukwa kuteroko nkudzivula.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamavula mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wako, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wako; pakuti thupi lao ndi lako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Usagonane ndi mdzukulu wako: mwana wa mwana wako wamwamuna kapena mwana wa mwana wako wamkazi. Kutero nʼkudzichotsa ulemu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamabvula mwana wamkazi wa mwana wamwamuna wako, kapena mwana wamkazi wa mwana wamkazi wako; pakuti thupi lao ndi lako.