Leviticus 18:11 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usagone ndi mwana wamkazi wa mkazi wa bambo wako amene bambo wakoyo adabala, poti ameneyo ndi mlongo wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamavula mwana wamkazi wa mkazi wa atate wako, amene anambala atate wako, ndiye mlongo wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Usagonane ndi mwana wamkazi wa mkazi wa abambo ako, amene abambo akowo anabereka; popeza ameneyo ndi mlongo wako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamabvula mwana wamkazi wa mkazi wa atate wako, amene anambala atate wako, ndiye mlongo wako.