Leviticus 18:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usagone ndi mkazi wa mbale wa bambo wako, poti ameneyo ndi mai wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamavula mbale wa atate wako; usamasendera kwa mkazi wake; ndiye mai wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Usachititse manyazi mchimwene wa abambo ako pogonana ndi mkazi wake popeza amenewo ndi azakhali ako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamabvula mbale wa atate wako; usamasendera kwa mkazi wace; ndiye mai wako.