Leviticus 18:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usagone ndi mkazi wa mwana wako, poti ameneyo ndi mpongozi wako.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamavula mpongozi wako; ndiye mkazi wa mwana wamwamuna wako; usamamvula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Usagonane ndi mpongozi wako popeza ameneyo ndi mkazi wa mwana wako. Choncho usamuchititse manyazi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamabvula mpongozi wako; ndiye mkazi wa mwana wamwamuna wako; usamambvula.