Leviticus 18:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Usayandikire mkazi kuti umvule pamene ali wosamba.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamasendera kwa mkazi kumvula pokhala ali padera chifukwa cha kudetsedwa kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Usamuyandikire mkazi kuti ugonane naye pa nthawi yake yosamba.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamasendera kwa mkazi kumbvula pokhala ali padera cifukwa ca kudetsedwa kwace.