Leviticus 18:20 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usagone ndi mkazi wa mnzako ndi kudziipitsa naye.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usagona naye mkazi wa mnansi wako, kudetsedwa naye limodzi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Usagonane ndi mkazi wa mnzako ndi kudziyipitsa naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usagona naye mkazi wa mnansi wako, kudetsedwa naye limodzi.