Leviticus 18:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Musadziipitse ndi zinthu zimenezi, chifukwa mitundu ina ya anthu amene ndikuipirikitsa inu mukubwera, idadziipitsa ndi zoipa zoterezi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamadzidetsa nacho chimodzi cha izi; pakuti amitundu amene ndiwapirikitsa pamaso panu amadetsedwa nazo zonsezi;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Musadzidetse ndi zinthu zimenezi chifukwa umo ndi mmene mitundu ina imene ndikuyithamangitsa pamaso panu inadzidetsera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamadzidetsa naco cimodzi ca izi; pakuti amitundu amene ndiwapitikitsa pamaso panu amadetsedwa nazo zonsezi;