Leviticus 18:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Dziko lidaipa kotero kuti ndidalanga tchimo lake, ndipo dzikolo lidasanza anthu ake okhalamo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
dziko lomwe lidetsedwa; chifukwa chake ndililanga, ndi dzikoli lisanza okhala m'mwemo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho dziko linayipa ndipo ndinalilanga chifukwa cha tchimo lake. Motero dzikolo linasanza anthu ake okhalamo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
dziko lomwe lidetsedwa; cifukwa cace ndililanga, ndi dzikoli lisanza okhala m'mwemo.