Leviticus 18:8 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Usachititse manyazi bambo wako pakugona ndi mkazi wake aliyense.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamavula mkazi wa atate wako; ndiye thupi la atate wako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Usagonane ndi mkazi wa abambo ako (osakhala amayi okubala). Ukatero ukuchititsa manyazi abambo ako.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamabvula mkazi wa atate wako; ndiye thupi la atate wako.