Leviticus 19:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musalumbire m'dzina langa monyenga ndi kumaipitsa dzina la Ine Mulungu wanu pakutero. Ine ndine Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamalumbira monama ndi kutchula dzina langa, ungaipse dzina la Mulungu wako; Ine ndine Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Musalumbire mʼdzina langa monyenga popeza kutero ndi kuyipitsa dzina la Mulungu wanu. Ine ndine Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamalumbira monama ndi kuchula dzina langa, ungaipse dzina la Mulungu wako; Ine ndine Yehova.