Leviticus 19:17 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Musadane ndi mbale wanu mumtima mwanu, koma mumdzudzule mosabisa kuti mungavomerezane naye pa tchimo lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamamuda mbale wako mumtima mwako; umdzudzule munthu mnzako ndithu, usadzitengera uchimo chifukwa cha iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Musamude mʼbale wanu mu mtima mwanu. Koma mudzudzuleni mnzanu moona mtima kuti musakhale wolakwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamamuda mbale wako mumtima mwako; umdzudzule munthu mnzako ndithu, usadzitengera ucimo cifukwa ca iye.