Leviticus 19:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Uza mpingo wonse wa Aisraele kuti, ‘Mukhale oyera pakuti Ine Chauta, Mulungu wanu, ndine woyera.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Nena ndi khamu lonse la ana a Israele, nuti nao, Muzikhala oyera; pakuti Ine ndine Yehova Mulungu wanu, ndine woyera.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“Uza gulu lonse la Aisraeli kuti, ‘Khalani oyera mtima chifukwa Ine, Yehova Mulungu wanu, ndine Woyera.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Nena ndi khamu lonse la ana a Israyeli, nuti nao, Muzikhala oyera; pakuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, ndine woyera.