Leviticus 19:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma pa chaka chachisanu mudzatha kudya zipatso zake, kuti choncho mitengoyo idzakubalireni kwambiri. Ine ndine Chauta, Mulungu wanu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chaka chachisanu muzidya zipatso zake, kuti zobala zake zikuchulukireni inu; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma chaka chachisanu, mudzatha kudya zipatso zake kuti mitengoyo idzakubalireni zochuluka. Ine ndine Yehova Mulungu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Caka cacisanu muzidya zipatso zace, kuti zobala zace zikucurukireni inu; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.