Leviticus 19:26 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Musadye nyama yamagazi. Musamaombeza kapena kuchita zaufiti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamadya kanthu ndi mwazi wake; musamachita nyanga, kapena kuombeza ula.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Musadye nyama ya magazi. “ ‘Musamawombeze kapena kuchita zamatsenga.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamadya kanthu ndi mwazi wace; musamacita nyanga, kapena kuombeza ula.