Leviticus 19:28 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musadzichekecheke pa thupi lanu chifukwa cha munthu wakufa kapena kudzitema mphini za mtundu uliwonse. Ine ndine Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamadzicheka matupi anu chifukwa cha akufa, kapena kutema mphini; Ine ndine Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Musadzichekecheke pathupi panu chifukwa cha munthu wakufa kapena kudzitema mphini pa thupi lanu. Ine ndine Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamadziceka matupi anu cifukwa ca akufa, kapena kutema mpbini; Ine ndine Yehova.