Leviticus 19:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Musaipitse mwana wanu wamkazi pakumsandutsa mkazi wachiwerewere kuti dziko lingasanduke la anthu adama ndi loipa kwambiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamaipsa mwana wako wamkazi ndi kumchititsa chigololo; lingadzale ndi chigololo dzikoli, ndi kudzazidwa nazo zochititsa manyazi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Musamuyipitse mwana wanu wamkazi pomusandutsa mkazi wachiwerewere. Mukatero dziko lidzasanduka la anthu achiwerewere ndi lodzaza ndi zoyipa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamaipsa mwana wako wamkazi ndi kumcititsa cigololo; lingadzale ndi cigololo dzikoli, ndi kudzazidwa nazo zocititsa manyazi.