Leviticus 19:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muzisunga masiku anga a Sabata ndi kulemekeza malo anga oyera, Ine ndine Chauta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Muzisunga masabata anga, ndi kuchitira ulemu malo anga opatulika; Ine ndine Yehova.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Muzisunga Masabata anga ndipo muzilemekeza malo anga opatulika. Ine ndine Yehova.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Muzisunga masabata anga, ndi kucitira ulemu malo anga opatulika; Ine ndine Yehova.