Leviticus 19:35 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Musamaweruza milandu molakwa, ndipo muyeso wanu woyesera utali wa zinthu, kulemera kwa zinthu kapena kuchuluka kwa zinthu, usamakhala wonyenga.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Musamachita chisalungamo poweruza mlandu, poyesa utali wake, kulemera kwake, kapena kuchuluka kwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Musamachite za chinyengo poweruza mlandu, kapena poyeza utali, kulemera ngakhalenso kuchuluka kwa zinthu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Musamacita cisalungamo poweruza mlandu, poyesa utali wace, kulemera kwace, kapena kucuruka kwace.