Leviticus 19:36 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Miyeso yanu ya sikelo, miyeso yoyesera kulemera kwa zinthu, miyeso yotchedwa efa ndi hini izikhala yolungama. Ine ndine Chauta, Mulungu wanu, amene ndidakutulutsani ku dziko la Ejipito.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mukhale nacho choyesera choona, miyeso yoona, efa woona, hini woona; Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakutulutsani m'dziko la Ejipito.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Miyeso ya sikelo, miyeso yoyezera kulemera kwa zinthu, miyeso yotchedwa efa ndi miyeso yotchedwa hini zikhale zolungama. Ine ndine Yehova, Mulungu wanu amene ndinakutulutsani ku dziko la Igupto.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mukhale naco coyesera coona, miyeso yoona, era woona, bini woona; Ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndinakuturutsani m'dziko la Aigupto.