Leviticus 19:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Muidye tsiku lomwe mwaiperekalo, kapena m'maŵa mwake, koma zotsalako mpaka pa tsiku lachitatu muzitenthe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lomwelo mwaipha, ndi m'mawa mwake muidye; ngati katsalirako kanthu tsiku lachitatu, muzikatentha ndi moto.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Nsembe izidyedwa tsiku lomwe mwayiperekalo kapena mmawa mwake. Chilichonse chotsala mpaka tsiku lachitatu chiyenera kutenthedwa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lomwelo mwaipha, ndi m'mawa mwace muidye; ngati katsalirako kanthu tsiku lacitatu, muzikatentha ndi moto.