Leviticus 19:9 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Pamene mukolola m'minda mwanu, musakolole munda wanu mpaka m'malire mwenimweni, ndipo musatolenso khunkha lake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pakukolola dzinthu za m'dziko mwanu, usamakololetsa m'mphepete mwa munda wako, nusamakunkha khunkha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Pamene mukolola zinthu mʼmunda mwanu musakolole mpaka mʼmphepete mwa munda, ndipo musatole khunkha lake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pakukolola dzinthu za m'dziko mwanu, usamakololetsa m'mphepete mwa munda wako, nusamakunkha khunkha.