Leviticus 2:1 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
“Munthu wina aliyense akabwera kudzapereka chopereka cha chakudya kwa Chauta, nsembeyo ikhale ya ufa wosalala. Ufawo authire mafuta ndi lubani,
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo munthu akabwera nacho chopereka ndicho nsembe yaufa ya kwa Yehova, chopereka chake chizikhala cha ufa wosalala; ndipo athirepo mafuta, ndi kuikapo lubani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Munthu wina aliyense akabwera ndi nsembe ya chakudya kwa Yehova, chopereka chake chizikhala ufa wosalala. Ufawo ausakanize ndi mafuta ndi lubani,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo munthu akabwera naco copereka ndico nsembe yaufa ya kwa Yehova, copereka cace cizikhala ca ufa wosalala; ndipo athirepo mafuta, ndi kuikapo libano.