Leviticus 2:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo nsembe yako ikakhala ya chopereka cha chakudya chophika pa chiwaya, chikhale ya ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo chopereka chako chikakhala nsembe yaufa ya mumphika, chikhale cha ufa wosalala ndi mafuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati nsembe yako yachakudya ndi yophikidwa pa chiwaya, ikhale ya buledi wa ufa wosalala wosakaniza ndi mafuta.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo copereka cako cikakhala nsembe yaufa ya mumphika, cikhale ca ufa wosalala ndi mafuta.