Leviticus 20:12 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu akagona ndi mkazi wa mwana wake, onsewo ayenera kuphedwa. Iwowo achita chigololo pachibale, ndipo magazi ao akhale pa iwowo.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu akagona ndi mpongozi wake, awaphe onse awiri; achita chisokonezo; mwazi wao ukhale pamtu pao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati munthu agonana ndi mkazi wa mwana wake, awiriwo ayenera kuphedwa. Iwo achita chinthu chonyansa kwambiri. Magazi awo adzakhala pa mitu pawo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu akagona ndi mpongozi wace, awaphe onse awiri; acita cisokonezo; mwazi wao ukhale pamtu pao.