Leviticus 20:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwamuna akagona ndi nyama, ayenera kuphedwa, ndipo nyamayo muiphenso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mwamuna akagona ndi nyama amuphe ndithu; muiphenso nyamayi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Ngati mwamuna agonana ndi nyama, iye ayenera kuphedwa, ndipo muyeneranso kupha nyamayo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mwamuna akagona ndi nyama amuphe ndithu; muiphenso nyamayi.