Leviticus 20:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Musavule mbale wa mai wanu kapena mlongo wa bambo wanu, poti kuteroko nkuvula wa pa chibale chanu. Onse aŵiriwo adzalipira machimo ao.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Usamavula mbale wa mai wako, kapena mlongo wa atate wako; popeza anavula abale ake; asenze mphulupulu yao.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Musagonane ndi mchemwali wa amayi anu kapena abambo anu, pakuti kutero ndi kuchititsa manyazi mʼbale wanu. Nonse mudzalipira mlandu wanu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Usamabvula mbale wa mai wako, kapena mlongo wa atate wako; popeza anabvula abale ace; asenze mphulupulu yao.