Leviticus 20:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Munthu akakwatira mkazi wa mbale wake, ndiye kuti wachita chinthu chonyansa. Wavula mbale wake, ndipo onse aŵiriwo adzakhala opanda ana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthu akatenga mkazi wa mbale wake, chodetsa ichi; wavula mbale wake; adzakhala osaona ana.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
“ ‘Munthu akakwatira mkazi wa mchimwene wake ndiye kuti wachita chinthu chonyansa. Wachititsa manyazi mʼbale wakeyo. Onse awiriwo adzakhala wopanda mwana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthu akatenga mkazi wa mbale wace, codetsa ici; wabvula mbale wace; adzakhala osaona ana.